5DM1 – WEKHA | LYRICS

Title: 5DM1 – Wekha 

[Pre-Chorus : Ninzo]

[Uli wekha wekha Mtima mwanga wekha wekha

Uli wekha wekha 

M’moyo mwanga wekha wekha]x2

[Chorus : Ninzo]

[Uli wekha wekha (m’moyo mwanga)

Uli wekha wekha (mu mtima mwanga)

Uli wekha wekha (m’dziko langa)

Uli wekha wekha (wekhaa)]x2

[Verse 1: Jay Cul]

Yah Sweet honey baby ndiwe wekhadi

Chikondi chako nthupi mwanga chikuwekhadi

yah umandimvetsa kukoma

Kundipangitsa kuyiwala zonse zokhoma

[Igha Elson]

You di only one my girl

Nobody take your place

You are mi number one girl yah (one)

Ask anything a go doit

Your love make me strong 

Pa iwe simdzachoka

[Chorus : Ninzo]

[Uli wekha wekha (m’moyo mwanga)

Uli wekha wekha (mu mtima mwanga)

Uli wekha wekha (m’dziko langa)

Uli wekha wekha (wekhaa)]×2

[Verse 2 : Ninzo]

Kaya ndinatani

Sinditha  kudya za magulu angapo (nuh)

Wekha ndiwe minister ndiwe president

Wekha wekha wekha usakhale pa easy

Olo jah jah amadalitsa anthu olimbika

[Ngwaxy]

Mutu umodzi sumazenza denga

Koma mtima wanga

Ndi iweyo unatenga  (ndee)

Ena azikumaka (moyo wanga) 

Wekha wekha honey

[Don Revil ]

265 

Go love you  no cheat

Til me die gyal 

You only In my life

You mi world gyal

You make my life so proud 

You real define the love

You gi mi everything anything 

Mi need in life

[Chorus : Ninzo]

[Uli wekha wekha (m’moyo mwanga)

Uli wekha wekha (mu mtima mwanga)

Uli wekha wekha (m’dziko langa)

Uli wekha wekha (wekhaa)]x2

[Bridge : Ninzo]

Mwanakazi ulipo wekha

Simdzakuleka iwe tadekha iwe

Mwanakazi ulipo wekha

Simdzakuleka iwe tadekha iwe

[Jay Cul]

Yah yah yah sumathawa 

Olo pa chilala

Chifukwa umadziwa kuti mawa kugwa mvula

Yah sumathawa olo athoke 

Chifukwa umadziwa kuti iwe ulipo wekha

  Yah  sumathawa 

pa chilala

Chifukwa umadziwa kuti mawa kugwa mvula

Yah sumathawa olo athoke 

Chifukwa umadziwa kuti iweyo ulipo wekha

[Outro : Jay Cul ]

Wekha wekha

Baby ulipo wekha

– – –

Lyrics by 5DM1

React & Share
Views:

RELATED POSTS

Scroll to Top